Levitiko 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pomaliza Mose anathira ena mwa mafuta odzozera pamutu pa Aroni nʼkumudzoza kuti akhale wopatulika.+
12 Pomaliza Mose anathira ena mwa mafuta odzozera pamutu pa Aroni nʼkumudzoza kuti akhale wopatulika.+