Ekisodo 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ubweretse Aroni ndi ana ake pakhomo la chihema chokumanako,+ ndipo uwasambitse* ndi madzi.+ Ekisodo 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako utenge mafuta odzozera+ nʼkuwathira pamutu pake kuti akhale wodzozedwa.+ Ekisodo 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako udzoze Aroni+ ndi ana ake+ ndipo uwayeretse kuti atumikire monga ansembe anga.+ Ekisodo 40:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ukatero udzaveke Aroni zovala zopatulika+ kenako nʼkumudzoza+ komanso kumuyeretsa ndipo adzatumikira monga wansembe wanga. Levitiko 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mkulu wa ansembe wokhala pakati pa abale ake ansembe, amene anamuthira mafuta odzozera unsembe pamutu pake,+ nʼkuikidwa kukhala wansembe* kuti azivala zovala zaunsembe,+ asalekerere tsitsi lake osalisamala ndipo asangʼambe zovala zake.+ Salimo 133:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zili ngati mafuta abwino amene athiridwa pamutu+Amene akuyenderera pandevu,Ndevu za Aroni,+Ndipo akuyenderera mpaka mʼkolala ya zovala zake.
13 Ukatero udzaveke Aroni zovala zopatulika+ kenako nʼkumudzoza+ komanso kumuyeretsa ndipo adzatumikira monga wansembe wanga.
10 Mkulu wa ansembe wokhala pakati pa abale ake ansembe, amene anamuthira mafuta odzozera unsembe pamutu pake,+ nʼkuikidwa kukhala wansembe* kuti azivala zovala zaunsembe,+ asalekerere tsitsi lake osalisamala ndipo asangʼambe zovala zake.+
2 Zili ngati mafuta abwino amene athiridwa pamutu+Amene akuyenderera pandevu,Ndevu za Aroni,+Ndipo akuyenderera mpaka mʼkolala ya zovala zake.