Ekisodo 40:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ukatero, udzaveke Aroni zovala zopatulika,+ kenako um’dzoze+ ndi kumuyeretsa kuti atumikire monga wansembe wanga.
13 Ukatero, udzaveke Aroni zovala zopatulika,+ kenako um’dzoze+ ndi kumuyeretsa kuti atumikire monga wansembe wanga.