Ekisodo 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ubweretse Aroni ndi ana ake pakhomo la chihema chokumanako,+ ndipo uwasambitse* ndi madzi.+ Ekisodo 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako utenge mafuta odzozera+ nʼkuwathira pamutu pake kuti akhale wodzozedwa.+