Ekisodo 26:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno uwombe nsalu yotchinga* khomo la chihema. Nsaluyo ikhale ya ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri.+ Ekisodo 40:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Atatero anaika nsalu yotchinga+ pakhomo la chihema. Levitiko 8:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Tenga Aroni limodzi ndi ana ake,+ zovala zawo,+ mafuta odzozera,+ ngʼombe yamphongo ya nsembe yamachimo, nkhosa ziwiri zamphongo ndi dengu la mikate yopanda zofufumitsa.+ 3 Ndiyeno usonkhanitse gulu lonse pakhomo la chihema chokumanako.”
36 Ndiyeno uwombe nsalu yotchinga* khomo la chihema. Nsaluyo ikhale ya ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri.+
2 “Tenga Aroni limodzi ndi ana ake,+ zovala zawo,+ mafuta odzozera,+ ngʼombe yamphongo ya nsembe yamachimo, nkhosa ziwiri zamphongo ndi dengu la mikate yopanda zofufumitsa.+ 3 Ndiyeno usonkhanitse gulu lonse pakhomo la chihema chokumanako.”