Levitiko 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pomaliza Mose anathira ena mwa mafuta odzozera pamutu pa Aroni nʼkumudzoza kuti akhale wopatulika.+ Salimo 133:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zili ngati mafuta abwino amene athiridwa pamutu+Amene akuyenderera pandevu,Ndevu za Aroni,+Ndipo akuyenderera mpaka mʼkolala ya zovala zake.
12 Pomaliza Mose anathira ena mwa mafuta odzozera pamutu pa Aroni nʼkumudzoza kuti akhale wopatulika.+
2 Zili ngati mafuta abwino amene athiridwa pamutu+Amene akuyenderera pandevu,Ndevu za Aroni,+Ndipo akuyenderera mpaka mʼkolala ya zovala zake.