Ekisodo 37:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Anapanganso mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika+ ndi mafuta onunkhira abwino kwambiri,+ osakanizidwa mwaluso.* 1 Mafumu 1:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndiyeno wansembe Zadoki anatenga nyanga ya mafuta+ mutenti+ nʼkudzoza Solomo.+ Zitatero anthuwo anayamba kuliza lipenga nʼkumafuula kuti: “Mfumu Solomo akhale ndi moyo wautali!” Salimo 89:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndapeza Davide mtumiki wanga,+Ndipo ndamudzoza ndi mafuta anga opatulika.+
29 Anapanganso mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika+ ndi mafuta onunkhira abwino kwambiri,+ osakanizidwa mwaluso.*
39 Ndiyeno wansembe Zadoki anatenga nyanga ya mafuta+ mutenti+ nʼkudzoza Solomo.+ Zitatero anthuwo anayamba kuliza lipenga nʼkumafuula kuti: “Mfumu Solomo akhale ndi moyo wautali!”