Ekisodo 30:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zinthu zimenezi upangire mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika, mafuta onunkhira osakanizidwa mwaluso.*+ Akhale mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika. Ekisodo 30:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Aliyense wopanga mafuta ofanana ndi amenewa, ndiponso amene angapake munthu wamba mafutawa, ayenera kuphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.’”+ Ekisodo 40:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako udzatenge mafuta odzozera+ nʼkudzoza chihema ndi zonse zimene zili mkati mwake+ ndipo udzachiyeretse pamodzi ndi ziwiya zake zonse kuti chikhale chopatulika.
25 Zinthu zimenezi upangire mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika, mafuta onunkhira osakanizidwa mwaluso.*+ Akhale mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika.
33 Aliyense wopanga mafuta ofanana ndi amenewa, ndiponso amene angapake munthu wamba mafutawa, ayenera kuphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.’”+
9 Kenako udzatenge mafuta odzozera+ nʼkudzoza chihema ndi zonse zimene zili mkati mwake+ ndipo udzachiyeretse pamodzi ndi ziwiya zake zonse kuti chikhale chopatulika.