Levitiko 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Mose anatenga mafuta odzozera nʼkudzoza chihema ndi zonse zimene zinali mkati mwake,+ kuti zikhale zopatulika. Numeri 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa tsiku limene Mose anamaliza kumanga chihema,+ anachidzoza+ nʼkuchipatula, limodzi ndi zipangizo zake zonse, guwa lansembe ndi ziwiya zake zonse.+ Atamaliza kudzoza ndi kupatula zinthu zimenezi,+
10 Ndiyeno Mose anatenga mafuta odzozera nʼkudzoza chihema ndi zonse zimene zinali mkati mwake,+ kuti zikhale zopatulika.
7 Pa tsiku limene Mose anamaliza kumanga chihema,+ anachidzoza+ nʼkuchipatula, limodzi ndi zipangizo zake zonse, guwa lansembe ndi ziwiya zake zonse.+ Atamaliza kudzoza ndi kupatula zinthu zimenezi,+