Ekisodo 30:26-28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mafuta amenewa udzozere chihema chokumanako,+ likasa la Umboni, 27 tebulo ndi ziwiya zake zonse, choikapo nyale ndi ziwiya zake zonse, guwa lansembe zofukiza, 28 guwa lansembe zopsereza ndi ziwiya zake zonse, komanso beseni ndi choikapo chake.
26 Mafuta amenewa udzozere chihema chokumanako,+ likasa la Umboni, 27 tebulo ndi ziwiya zake zonse, choikapo nyale ndi ziwiya zake zonse, guwa lansembe zofukiza, 28 guwa lansembe zopsereza ndi ziwiya zake zonse, komanso beseni ndi choikapo chake.