Ekisodo 40:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako udzatenge mafuta odzozera+ nʼkudzoza chihema ndi zonse zimene zili mkati mwake+ ndipo udzachiyeretse pamodzi ndi ziwiya zake zonse kuti chikhale chopatulika. Numeri 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa tsiku limene Mose anamaliza kumanga chihema,+ anachidzoza+ nʼkuchipatula, limodzi ndi zipangizo zake zonse, guwa lansembe ndi ziwiya zake zonse.+ Atamaliza kudzoza ndi kupatula zinthu zimenezi,+
9 Kenako udzatenge mafuta odzozera+ nʼkudzoza chihema ndi zonse zimene zili mkati mwake+ ndipo udzachiyeretse pamodzi ndi ziwiya zake zonse kuti chikhale chopatulika.
7 Pa tsiku limene Mose anamaliza kumanga chihema,+ anachidzoza+ nʼkuchipatula, limodzi ndi zipangizo zake zonse, guwa lansembe ndi ziwiya zake zonse.+ Atamaliza kudzoza ndi kupatula zinthu zimenezi,+