Ekisodo 40:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno udzatenge mafuta odzozera+ ndi kudzoza chihema chopatulika ndi zonse zimene zili mkati mwake.+ Motero udzachiyeretse pamodzi ndi ziwiya zake zonse kuti chikhale chopatulika.
9 Ndiyeno udzatenge mafuta odzozera+ ndi kudzoza chihema chopatulika ndi zonse zimene zili mkati mwake.+ Motero udzachiyeretse pamodzi ndi ziwiya zake zonse kuti chikhale chopatulika.