Ekisodo 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Mose anapita kwa anthu nʼkuwafotokozera mawu onse a Yehova ndi zigamulo zake zonse.+ Atatero anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Mawu onse amene Yehova wanena tidzachita.”+ Deuteronomo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mʼchaka cha 40,+ mʼmwezi wa 11, pa tsiku loyamba la mweziwo, Mose anauza Aisiraeli* zonse zimene Yehova anamuuza kuti awauze.
3 Ndiyeno Mose anapita kwa anthu nʼkuwafotokozera mawu onse a Yehova ndi zigamulo zake zonse.+ Atatero anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Mawu onse amene Yehova wanena tidzachita.”+
3 Mʼchaka cha 40,+ mʼmwezi wa 11, pa tsiku loyamba la mweziwo, Mose anauza Aisiraeli* zonse zimene Yehova anamuuza kuti awauze.