Levitiko 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano lamulo la nsembe yambewu+ ndi ili: Ana a Aroni azibweretsa nsembeyi pamaso pa Yehova patsogolo pa guwa lansembe. Levitiko 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pophika, musaikemo zofufumitsa zilizonse.+ Ndaupereka monga gawo lawo kuchokera pansembe zanga zowotcha pamoto.+ Zimenezi nʼzopatulika koposa+ mofanana ndi nsembe yamachimo komanso nsembe yakupalamula.
14 Tsopano lamulo la nsembe yambewu+ ndi ili: Ana a Aroni azibweretsa nsembeyi pamaso pa Yehova patsogolo pa guwa lansembe.
17 Pophika, musaikemo zofufumitsa zilizonse.+ Ndaupereka monga gawo lawo kuchokera pansembe zanga zowotcha pamoto.+ Zimenezi nʼzopatulika koposa+ mofanana ndi nsembe yamachimo komanso nsembe yakupalamula.