Ekisodo 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Muzibweretsa kunyumba ya Yehova Mulungu wanu zipatso zoyamba kucha zamʼminda yanu zomwe ndi zabwino kwambiri.+ Musamawiritse mwana wa mbuzi mumkaka wa mayi ake.+ Numeri 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Muzikapereka mikate yozungulira yoboola pakati ya ufa wamisere kuti ikhale chopereka cha zipatso zoyambirira kucha.+ Muzikaipereka ngati mmene mumaperekera chopereka chochokera popunthira mbewu. 2 Mbiri 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Aisiraeli atangomva zimenezi, anapereka zinthu zambiri zoyambirira kukolola monga mbewu, vinyo watsopano, mafuta,+ uchi ndi zokolola zonse zakumunda+ ndipo anapereka mowolowa manja chakhumi cha zinthu zonse.+ Miyambo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Uzilemekeza Yehova ndi zinthu zako zamtengo wapatali+Ndiponso ndi zipatso zako zonse zoyambirira.*+
19 Muzibweretsa kunyumba ya Yehova Mulungu wanu zipatso zoyamba kucha zamʼminda yanu zomwe ndi zabwino kwambiri.+ Musamawiritse mwana wa mbuzi mumkaka wa mayi ake.+
20 Muzikapereka mikate yozungulira yoboola pakati ya ufa wamisere kuti ikhale chopereka cha zipatso zoyambirira kucha.+ Muzikaipereka ngati mmene mumaperekera chopereka chochokera popunthira mbewu.
5 Aisiraeli atangomva zimenezi, anapereka zinthu zambiri zoyambirira kukolola monga mbewu, vinyo watsopano, mafuta,+ uchi ndi zokolola zonse zakumunda+ ndipo anapereka mowolowa manja chakhumi cha zinthu zonse.+
9 Uzilemekeza Yehova ndi zinthu zako zamtengo wapatali+Ndiponso ndi zipatso zako zonse zoyambirira.*+