Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 14:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pa tsiku la 7 azimeta tsitsi lake lonse lakumutu, ndevu zake zonse ndi nsidze zonse. Akamaliza kumeta tsitsi lake lonse azichapa zovala zake nʼkusamba mʼmadzi ndipo adzakhala woyera.

  • Maliko 1:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Anamuuza kuti: “Samala, usauze aliyense zimenezi, koma upite ukadzionetse kwa wansembe ndipo chifukwa chakuti wayeretsedwa, ukapereke zinthu zimene Mose analamula,+ kuti ukhale umboni kwa iwo.”+

  • Luka 5:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kenako analamula munthuyo kuti asauze aliyense. Ndiyeno anamuuza kuti: “Koma upite ukadzionetse kwa wansembe, ndipo ukapereke nsembe ya kuyeretsedwa kwako, monga mmene Mose analamulira,+ kuti ikhale umboni kwa iwo.”+

  • Luka 17:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Yesu atawaona anawauza kuti: “Pitani mukadzionetse kwa ansembe.”+ Ndiyeno pamene ankapita anayeretsedwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena