Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 11:24, 25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Zamoyo zimenezi nʼzimene mungadzidetse nazo. Aliyense wokhudza zamoyo zimenezi zitafa adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.+ 25 Aliyense wonyamula chilichonse mwa zamoyo zimenezi chitafa, azichapa zovala zake,+ ndipo adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.

  • Levitiko 14:46, 47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Koma aliyense wolowa mʼnyumbayo pa masiku amene wansembe walamula kuti munthu asalowemo,+ azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.+ 47 Aliyense amene wagona mʼnyumbamo ndiponso aliyense amene wadyeramo chakudya azichapa zovala zake.

  • Levitiko 17:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ngati munthu aliyense wadya nyama imene waipeza yakufa kapena imene yaphedwa ndi chilombo,+ kaya akhale nzika kapena mlendo wokhala pakati panu, munthu ameneyo azichapa zovala zake nʼkusamba thupi lonse, ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.+ Kenako azikhala woyera.

  • Levitiko 22:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Munthu wokhudza chilichonse mwa zinthu zoterezi azikhala wodetsedwa mpaka madzulo ndipo asamadye chinthu chopatulika chilichonse, koma azisamba thupi lonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena