Ekisodo 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anauza anthuwo kuti: “Pofika tsiku lachitatu mukhale okonzeka. Amuna asagone ndi akazi awo.”* 1 Samueli 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Davide anayankha wansembeyo kuti: “Akazi sanatiyandikire ngati mmene zinalilinso poyamba pamene ndinapita kukamenya nkhondo.+ Anyamatawo amakhala oyera ngakhale pamene tili pa ntchito wamba, ndiye kuli bwanji lero?”
5 Davide anayankha wansembeyo kuti: “Akazi sanatiyandikire ngati mmene zinalilinso poyamba pamene ndinapita kukamenya nkhondo.+ Anyamatawo amakhala oyera ngakhale pamene tili pa ntchito wamba, ndiye kuli bwanji lero?”