Levitiko 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Ngati mwamuna ali ndi nthenda ya kukha kumaliseche, nthenda yakeyo ikumupangitsa kukhala wodetsedwa.+ Levitiko 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mkazi akakha magazi kwa masiku ambiri+ pamene si nthawi yake yosamba,+ kapena akapitiriza kukha magazi nthawi yake yosamba itatha, azikhala wodetsedwa masiku onse amene akukha magaziwo ngati mmene amakhalira pa nthawi yake yosamba.
2 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Ngati mwamuna ali ndi nthenda ya kukha kumaliseche, nthenda yakeyo ikumupangitsa kukhala wodetsedwa.+
25 Mkazi akakha magazi kwa masiku ambiri+ pamene si nthawi yake yosamba,+ kapena akapitiriza kukha magazi nthawi yake yosamba itatha, azikhala wodetsedwa masiku onse amene akukha magaziwo ngati mmene amakhalira pa nthawi yake yosamba.