Aheberi 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho zinali zofunika kuti zifaniziro+ za zinthu zakumwamba ziyeretsedwe mʼnjira imeneyi.+ Koma zinthu zakumwamba zenizenizo zimafunika kuyeretsedwa ndi nsembe zabwino kuposa zimenezi.
23 Choncho zinali zofunika kuti zifaniziro+ za zinthu zakumwamba ziyeretsedwe mʼnjira imeneyi.+ Koma zinthu zakumwamba zenizenizo zimafunika kuyeretsedwa ndi nsembe zabwino kuposa zimenezi.