19 Ena mwa magaziwo aziwadonthezera paguwalo ndi chala chake maulendo 7, kuti likhale lopatulika komanso kuti aliyeretse ku zinthu zodetsa za Aisiraeli.
20 Akamaliza kuphimbira machimo+ malo oyera, chihema chokumanako ndi guwa lansembe,+ azibweretsanso mbuzi yamoyo ija.+