Levitiko 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Aroni azichita maere pa mbuzi ziwirizo. Maere amodzi akhale a Yehova, ndipo ena akhale a mbuzi yotenga machimo a anthu.* Levitiko 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma mbuzi imene maere asonyeza kuti ndi yotenga machimo a anthu, aziibweretsa yamoyo nʼkuiimika pamaso pa Yehova kuti machimo a anthu aphimbidwe. Akatero aziitumiza mʼchipululu monga mbuzi yotenga machimo a anthu.+
8 Ndiyeno Aroni azichita maere pa mbuzi ziwirizo. Maere amodzi akhale a Yehova, ndipo ena akhale a mbuzi yotenga machimo a anthu.*
10 Koma mbuzi imene maere asonyeza kuti ndi yotenga machimo a anthu, aziibweretsa yamoyo nʼkuiimika pamaso pa Yehova kuti machimo a anthu aphimbidwe. Akatero aziitumiza mʼchipululu monga mbuzi yotenga machimo a anthu.+