Levitiko 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma mbuzi imene maere asonyeza kuti ndi ya Azazeli, aziiimika yamoyo pamaso pa Yehova kuti aiphimbire machimo. Akatero aziitumiza+ m’chipululu monga ya Azazeli.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:10 Nsanja ya Olonda,3/1/1989, ptsa. 16-17
10 Koma mbuzi imene maere asonyeza kuti ndi ya Azazeli, aziiimika yamoyo pamaso pa Yehova kuti aiphimbire machimo. Akatero aziitumiza+ m’chipululu monga ya Azazeli.+