Levitiko 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako wansembe azidontheza+ magaziwo maulendo 7+ pamunthu amene akudziyeretsa ku khateyo, ndipo azigamula kuti munthuyo ndi woyera.+ Akatero, aziulutsa mbalame yamoyo ija pabwalo.+
7 Kenako wansembe azidontheza+ magaziwo maulendo 7+ pamunthu amene akudziyeretsa ku khateyo, ndipo azigamula kuti munthuyo ndi woyera.+ Akatero, aziulutsa mbalame yamoyo ija pabwalo.+