2 Mafumu 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Elisa anatuma mthenga kukamuuza kuti: “Pita ukasambe+ maulendo 7+ mumtsinje wa Yorodano, kuti mnofu wako ubwerere mwakale ndi kuti iweyo+ ukhale woyera.”
10 Koma Elisa anatuma mthenga kukamuuza kuti: “Pita ukasambe+ maulendo 7+ mumtsinje wa Yorodano, kuti mnofu wako ubwerere mwakale ndi kuti iweyo+ ukhale woyera.”