Levitiko 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako wansembe azidontheza+ magaziwo maulendo 7+ pamunthu amene akudziyeretsa ku khateyo, ndipo azigamula kuti munthuyo ndi woyera.+ Akatero, aziulutsa mbalame yamoyo ija pabwalo.+ Numeri 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako, wansembe Eleazara atengeko magazi a ng’ombeyo ndi chala chake, n’kuwawaza maulendo 7 moyang’anizana ndi chihema chokumanako.+
7 Kenako wansembe azidontheza+ magaziwo maulendo 7+ pamunthu amene akudziyeretsa ku khateyo, ndipo azigamula kuti munthuyo ndi woyera.+ Akatero, aziulutsa mbalame yamoyo ija pabwalo.+
4 Kenako, wansembe Eleazara atengeko magazi a ng’ombeyo ndi chala chake, n’kuwawaza maulendo 7 moyang’anizana ndi chihema chokumanako.+