Levitiko 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mbuziyo izinyamula zolakwa zawo zonse+ pamutu pake ndipo aziitumiza kuchipululu.+ Salimo 103:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Monga mmene kum’mawa kwatalikirana ndi kumadzulo,+Momwemonso, watiikira kutali zolakwa zathu.+