Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 16:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma mbuzi imene maere asonyeza kuti ndi ya Azazeli, aziiimika yamoyo pamaso pa Yehova kuti aiphimbire machimo. Akatero aziitumiza+ m’chipululu monga ya Azazeli.+

  • Salimo 103:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Monga mmene kum’mawa kwatalikirana ndi kumadzulo,+

      Momwemonso, watiikira kutali zolakwa zathu.+

  • Ezekieli 18:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Zolakwa zonse zimene anachita sizidzakumbukiridwa ndipo sadzalangidwa nazo.+ Adzakhalabe ndi moyo chifukwa cha zinthu zolungama zimene anachita.’+

  • Mika 7:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Inu mudzatichitiranso chifundo+ ndipo mudzapondaponda zolakwa zathu.+ Machimo athu onse mudzawaponya pakati pa nyanja yozama.+

  • Aheberi 13:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Zinalinso chimodzimodzi ndi Yesu. Kuti ayeretse+ anthu ndi magazi ake,+ anakavutikira kunja kwa chipata.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena