Levitiko 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma mbuzi imene maere asonyeza kuti ndi yotenga machimo a anthu, aziibweretsa yamoyo nʼkuiimika pamaso pa Yehova kuti machimo a anthu aphimbidwe. Akatero aziitumiza mʼchipululu monga mbuzi yotenga machimo a anthu.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:10 Nsanja ya Olonda,3/1/1989, ptsa. 16-17
10 Koma mbuzi imene maere asonyeza kuti ndi yotenga machimo a anthu, aziibweretsa yamoyo nʼkuiimika pamaso pa Yehova kuti machimo a anthu aphimbidwe. Akatero aziitumiza mʼchipululu monga mbuzi yotenga machimo a anthu.+