Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 33:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Manase anayamba kupemphera kwa Mulungu ndipo iye anamva kupembedzera kwake+ ndi pempho lake lopempha chifundo. Kenako anam’bwezera ku Yerusalemu ku ufumu wake,+ ndipo Manase anadziwa kuti Yehova ndiye Mulungu woona.+

  • Salimo 25:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Musakumbukire machimo a pa unyamata wanga ndi zolakwa zanga.+

      Ndikumbukireni malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha,+

      Ndiponso chifukwa cha ubwino wanu, inu Yehova.+

  • Yesaya 43:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 “Ineyo ndi amene ndikufafaniza+ zolakwa zako,+ ndipo machimo ako sindidzawakumbukiranso.+

  • Ezekieli 33:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Palibe tchimo ngakhale limodzi mwa machimo onse amene anachita limene lidzakumbukiridwe ndi kumulanga nalo.+ Iye anachita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo. Choncho adzakhalabe ndi moyo.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena