2 Mbiri 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 inu mumve muli kumwamba+ ndipo muchitepo kanthu+ mwa kusonyeza amene ali wolakwa pom’bwezera temberero lake,+ ndi kusonyeza amene ali wolungama+ pom’patsa mphoto malinga ndi chilungamo chake.+
23 inu mumve muli kumwamba+ ndipo muchitepo kanthu+ mwa kusonyeza amene ali wolakwa pom’bwezera temberero lake,+ ndi kusonyeza amene ali wolungama+ pom’patsa mphoto malinga ndi chilungamo chake.+