Levitiko 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Musachoke pakhomo la chihema chokumanako kwa masiku 7, mpaka masiku okuikani kuti mukhale ansembe atatha, chifukwa padzatenga masiku 7 kuti muikidwe kukhala ansembe.+
33 Musachoke pakhomo la chihema chokumanako kwa masiku 7, mpaka masiku okuikani kuti mukhale ansembe atatha, chifukwa padzatenga masiku 7 kuti muikidwe kukhala ansembe.+