Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 25:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pasapezeke aliyense pakati panu wochitira mnzake chinyengo,+ ndipo muziopa Mulungu wanu,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.+

  • Nehemiya 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Abwanamkubwa amene analipo ine ndisanakhale, ankalemetsa anthu ndipo tsiku lililonse ankalandira masekeli* 40 asiliva ogulira chakudya ndi vinyo. Komanso atumiki awo ankapondereza anthu. Koma ine sindinachite zimenezo+ chifukwa choopa Mulungu.+

  • Miyambo 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Kuopa Yehova ndi chiyambi cha kudziwa zinthu.+

      Zitsiru zokha ndi zimene zimanyoza nzeru komanso malangizo.+

  • Miyambo 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+

      Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso mawu achinyengo.+

  • 1 Petulo 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Muzilemekeza anthu amitundu yonse.+ Muzikonda gulu lonse la abale,+ muziopa Mulungu+ komanso muzilemekeza mfumu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena