2 “Aisiraeli akonze nsembe ya Pasika+ pa nthawi yake imene inaikidwiratu.+ 3 Pa tsiku la 14 la mwezi uno, madzulo kuli kachisisira, mudzakonze nsembeyo pa nthawi yake yoikidwiratu. Mudzaikonze motsatira malamulo ake onse ndiponso njira zonse za kakonzedwe kake.”+