Nehemiya 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno tsiku lililonse, kuyambira tsiku loyamba mpaka lomaliza, ankawerenga mokweza buku la Chilamulo cha Mulungu woona.+ Anachita chikondwererochi masiku 7 ndipo pa tsiku la 8 anachita msonkhano wapadera mogwirizana ndi Chilamulo.+
18 Ndiyeno tsiku lililonse, kuyambira tsiku loyamba mpaka lomaliza, ankawerenga mokweza buku la Chilamulo cha Mulungu woona.+ Anachita chikondwererochi masiku 7 ndipo pa tsiku la 8 anachita msonkhano wapadera mogwirizana ndi Chilamulo.+