Levitiko 23:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Tsiku la 15 la mwezi wa 7 umenewu, ndi tsiku lochitira Yehova Chikondwerero cha Misasa kwa masiku 7.+ Levitiko 23:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kwa masiku 7 muzipereka nsembe yowotcha pamoto kwa Yehova. Pa tsiku la 8 muzichita msonkhano wopatulika,+ ndipo muzipereka nsembe yowotcha pamoto kwa Yehova. Umenewu ndi msonkhano wapadera. Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa.
34 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Tsiku la 15 la mwezi wa 7 umenewu, ndi tsiku lochitira Yehova Chikondwerero cha Misasa kwa masiku 7.+
36 Kwa masiku 7 muzipereka nsembe yowotcha pamoto kwa Yehova. Pa tsiku la 8 muzichita msonkhano wopatulika,+ ndipo muzipereka nsembe yowotcha pamoto kwa Yehova. Umenewu ndi msonkhano wapadera. Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa.