Numeri 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa tsiku la 15 la mwezi wa 7, muzichita msonkhano wopatulika. Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa. Muzichita chikondwerero posonyeza kulemekeza Yehova masiku 7.+
12 Pa tsiku la 15 la mwezi wa 7, muzichita msonkhano wopatulika. Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa. Muzichita chikondwerero posonyeza kulemekeza Yehova masiku 7.+