Ekisodo 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndipatulireni* mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu ndi wa chiweto, pakati pa Aisiraeli. Ameneyu ndi wanga.”+ Ekisodo 34:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa* ndi wanga,+ kuphatikizapo mwana woyamba kubadwa wa ziweto zanu zonse, kaya ndi mwana woyamba kubadwa wa ngʼombe kapena nkhosa.+ Numeri 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chamoyo chilichonse choyamba kubadwa+ chimene azipereka kwa Yehova, kaya ndi munthu kapena nyama, chizikhala chako. Komabe uzionetsetsa kuti wawombola mwana woyamba kubadwa wa munthu+ komanso mwana woyamba kubadwa wa nyama yodetsedwa.+ Luka 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Izi zinali zogwirizana ndi zimene zinalembedwa mʼChilamulo cha Yehova* kuti: “Mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa* adzakhala woyera kwa Yehova.”*+
2 “Ndipatulireni* mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu ndi wa chiweto, pakati pa Aisiraeli. Ameneyu ndi wanga.”+
19 Mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa* ndi wanga,+ kuphatikizapo mwana woyamba kubadwa wa ziweto zanu zonse, kaya ndi mwana woyamba kubadwa wa ngʼombe kapena nkhosa.+
15 Chamoyo chilichonse choyamba kubadwa+ chimene azipereka kwa Yehova, kaya ndi munthu kapena nyama, chizikhala chako. Komabe uzionetsetsa kuti wawombola mwana woyamba kubadwa wa munthu+ komanso mwana woyamba kubadwa wa nyama yodetsedwa.+
23 Izi zinali zogwirizana ndi zimene zinalembedwa mʼChilamulo cha Yehova* kuti: “Mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa* adzakhala woyera kwa Yehova.”*+