Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Ndipatulireni* mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu ndi wa chiweto, pakati pa Aisiraeli. Ameneyu ndi wanga.”+

  • Levitiko 27:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Koma munthu asapereke nyama iliyonse yoyamba kubadwa kuti ikhale yopatulika, chifukwa iliyonse yoyamba kubadwa ndi ya Yehova.+ Kaya ndi ngʼombe kapena nkhosa, ndi za Yehova.+

  • Numeri 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mwana aliyense woyamba kubadwa ndi wanga.+ Pa tsiku limene ndinapha mwana aliyense woyamba kubadwa mʼdziko la Iguputo,+ ndinapatula mwana aliyense woyamba kubadwa pakati pa Aisiraeli kuti akhale wanga, kuyambira munthu mpaka chiweto.+ Amenewa azikhala anga. Ine ndine Yehova.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena