-
Ezekieli 46:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Mʼmawa uliwonse, iwo azipereka kwa ansembe mwana wa nkhosa wamphongo, nsembe yambewu komanso mafuta, kuti zikhale nsembe yopsereza yathunthu ya nthawi zonse.’
-