-
Ekisodo 29:39, 40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Uzipereka mwana wa nkhosa mmodzi mʼmawa, ndipo mwana wa nkhosa winayo madzulo kuli kachisisira.*+ 40 Popereka mwana wa nkhosa woyamba, uzipereka limodzi ndi ufa wosalala, muyezo wake gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa efa,* wothira mafuta oyenga bwino kwambiri okwana gawo limodzi mwa magawo 4 a muyezo wa hini,* ndi gawo limodzi mwa magawo 4 a vinyo wa nsembe yachakumwa.
-