40 Popereka mwana wa nkhosa woyamba, uzipereka limodzi ndi ufa wosalala,+ muyezo wake gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa efa, wothira mafuta oyenga bwino kwambiri okwana gawo limodzi mwa magawo anayi a muyezo wa hini, ndi gawo limodzi mwa magawo anayi a vinyo wa nsembe yachakumwa.+