Levitiko 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nsembe yambewu imene mukupereka kwa Yehova isakhale ndi zofufumitsa,+ chifukwa simukuyenera kuwotcha ufa wokanda wokhala ndi zofufumitsa kapena uchi,* ngati nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova.
11 Nsembe yambewu imene mukupereka kwa Yehova isakhale ndi zofufumitsa,+ chifukwa simukuyenera kuwotcha ufa wokanda wokhala ndi zofufumitsa kapena uchi,* ngati nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova.