Numeri 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ngati mukupereka ngʼombe yamphongo kuti ikhale nsembe yopsereza,+ kapena nsembe imene mukuipereka chifukwa cha lonjezo lapadera,+ kapenanso kuti ikhale nsembe yamgwirizano kwa Yehova,+ Numeri 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiponso muzikapereka vinyo kuti akhale nsembe yachakumwa.+ Vinyoyo azikakhala wokwana hafu ya muyezo wa hini. Akakhale nsembe yowotcha pamoto, yakafungo kosangalatsa* kwa Yehova.
8 Koma ngati mukupereka ngʼombe yamphongo kuti ikhale nsembe yopsereza,+ kapena nsembe imene mukuipereka chifukwa cha lonjezo lapadera,+ kapenanso kuti ikhale nsembe yamgwirizano kwa Yehova,+
10 Ndiponso muzikapereka vinyo kuti akhale nsembe yachakumwa.+ Vinyoyo azikakhala wokwana hafu ya muyezo wa hini. Akakhale nsembe yowotcha pamoto, yakafungo kosangalatsa* kwa Yehova.