Levitiko 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muziwerenga masiku 50+ kukafika pa tsiku lotsatizana ndi tsiku limene Sabata la 7 lathera, kenako muzipereka nsembe yambewu zatsopano kwa Yehova.+ Levitiko 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Muziperekanso mwana wa mbuzi mmodzi monga nsembe yamachimo,+ ndi ana a nkhosa amphongo awiri, aliyense wachaka chimodzi, monga nsembe yamgwirizano.+
16 Muziwerenga masiku 50+ kukafika pa tsiku lotsatizana ndi tsiku limene Sabata la 7 lathera, kenako muzipereka nsembe yambewu zatsopano kwa Yehova.+
19 Muziperekanso mwana wa mbuzi mmodzi monga nsembe yamachimo,+ ndi ana a nkhosa amphongo awiri, aliyense wachaka chimodzi, monga nsembe yamgwirizano.+