Numeri 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Upange malipenga awiri+ asiliva. Uchite kusula, ndipo uziwagwiritsa ntchito poitanitsa msonkhano komanso posamutsa msasa. Salimo 81:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa tsiku limene mwezi watsopano waoneka,+ imbani lipenga la nyanga ya nkhosa,Pa tsiku limene mwezi wathunthu waoneka, imbani lipenga la nyanga ya nkhosa, limene limaimbidwa pa tsiku la chikondwerero.+
2 “Upange malipenga awiri+ asiliva. Uchite kusula, ndipo uziwagwiritsa ntchito poitanitsa msonkhano komanso posamutsa msasa.
3 Pa tsiku limene mwezi watsopano waoneka,+ imbani lipenga la nyanga ya nkhosa,Pa tsiku limene mwezi wathunthu waoneka, imbani lipenga la nyanga ya nkhosa, limene limaimbidwa pa tsiku la chikondwerero.+