Numeri 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Upange malipenga+ awiri asiliva. Uchite kusula, ndipo uziwagwiritsa ntchito poitanitsa+ msonkhano ndi posamutsa msasa. Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),6/2020, tsa. 30 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), ptsa. 2162-2163
2 “Upange malipenga+ awiri asiliva. Uchite kusula, ndipo uziwagwiritsa ntchito poitanitsa+ msonkhano ndi posamutsa msasa.