-
Numeri 4:38-40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Ana a Gerisoni+ anawerengedwa potengera mabanja awo ndi nyumba za makolo awo, 39 anawerenga onse kuyambira azaka 30 mpaka 50, amene anali mʼgulu la anthu amene anasankhidwa kuti azitumikira pachihema chokumanako. 40 Onse amene anawerengedwa potengera mabanja awo ndi nyumba za makolo awo, anakwana 2,630.+
-