Numeri 4:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 amene anawerengedwa malinga ndi mabanja awo, potsata nyumba za makolo awo, onse pamodzi anakwana 2,630.+
40 amene anawerengedwa malinga ndi mabanja awo, potsata nyumba za makolo awo, onse pamodzi anakwana 2,630.+