Numeri 4:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Onse amene anawerengedwa potengera mabanja awo ndi nyumba za makolo awo, anakwana 2,630.+